democracy ndimene imatipweteka chifukwa anthu amene akuononga dzikoli timawadziwa but we choose being quiet zomwe zimapangisa kuti a ndale akhale ndi mphamvu kwambiri
2026-10-28 19:42:34
1
rodneykulinji🇲🇼 :
He's more intelligent than 5 Members of Parliament adding them together
2026-10-29 05:43:13
0
Justin peter :
amphawi amakhala ndi mzeru
2026-10-29 06:03:20
0
Kiddy7@28 :
Real economists alibe zochita amayendesa makabaza, kuphika zigege...i mean anthu ofunika kukhala ma position ambili tilibe kuthekera.....
2026-10-28 17:25:44
1
mdzudzuli Yusufu chidolanthaka :
zoonadi big
2026-10-28 10:04:58
1
Chiccondi Yahcee Bg Vhutho :
ichichi musachione kusasamba ayi ndithu ndichosamba mumtima ndi mzeru zomwe ichichi or chitapatsidwa udindo is worth it
2026-10-27 09:04:13
23
Martin Brian Kwalira🇲🇼🇲🇼 :
This guy knows economics. But people seeing his appearance thinking he doesn't have sense. But this guy given opportunity can do better
2026-10-27 21:26:42
15
Philemon Mwakilama :
ndiwe Dolo
2026-10-28 19:03:01
1
Madalitso white :
this video will not get old
2026-10-28 13:34:41
7
Ndawina K Chamwaka🇲🇼 :
Anthu wamba titati tiziganiza chonchi then we can vote for Denis Mahata....the only hope for Malawi who wants to bring total change.
2026-10-27 08:11:38
17
Xhosa :
Ntangova GDP ndinaziwa zinthu chikuzisata
2026-10-27 17:54:56
15
fortune :
ada awa tingawapeze bwanji
2026-10-27 17:07:05
7
EDDRISAH NYONDO :
The true definition of don’t judge a book by its cover. Uyu munthu mufufuzeni akhale mulangizi wa president pa nkhani za uyowo wa anthu ndizina
2026-10-27 09:40:07
12
madridstar :
adha awa ndi genius.. economist weni weni[Pray]
2026-10-27 06:13:11
8
Nyoze Banda :
ku lankhula zowona
2026-10-27 07:54:24
7
That guy bless265 :
dziko ili democracy ai ai tati ....iiiii ma guy ada awaa afunika ya fanta ndan uyuu😂😂😂😂🙌🙌🙌🙌🙌🔥🔥🔥🔥👌👌👌👌
2026-10-27 11:52:38
6
jojo :
Most intelligent man ever in Malawi
2026-10-27 13:51:50
9
Stonard Kunje :
pdt nd chan kod
2026-10-28 09:35:52
1
Aaron unique silo :
he knows GDP,this can can preach sense
2026-10-27 12:01:56
9
Ruth Chatha :
anthu mulindi nzeru lero ndi izi😭😭😭😭😭
2026-10-27 09:32:27
5
NAMASEKO :
ndichi Yazaa 🔥🔥🔥
2026-10-28 20:10:47
3
kamutukambewa :
nde anati amene abwereyo adzakhala oipitsitsa kwambiri ....ndekut fundo zake democracy nzolondola...pamene tikusemphani ndi ine mpakati kukwanitsa kudyesa uosaka koma akanati apezenjira kut osauka azizipezera zakudya in so doing change izichitika koma kumangowadyetsa nothing will change ..tizingoyankhula fundo zanzeru koma dziko osatsintha ,zikomo kumpando
2026-10-27 12:31:24
2
Burj Khalifa_🇦🇪 :
comment section yose akudziwa GDP ndi anthu 5 okha😂😅😅😂
2026-10-28 09:27:03
3
JALAKE MW superstar :
Denis mahata🔥🔥🔥🔥🔥
2026-10-27 18:39:13
4
Blessings Fernando87 :
mpaka GDP
2026-10-28 10:16:05
2
To see more videos from user @macksonjuniorhara, please go to the Tikwm
homepage.