mnakozeka kt ndiike status km kumapetoko 😂😂😂ndigwetsedwa kumpingo🤸
2026-10-29 06:30:39
36
chisper😌🌺 :
at first ndimava kuti okondedwa suzapeza mtendere mpaka ambuye yesu azabwera🤣
2026-11-11 12:53:50
5
Sammie🌹 :
ndili pachibwezi ndi amuna anga anadzathetsa chibwezi koma ine kulira mpakana osamadya, kuwauza mai anga kuti awauze andigoneka kuchipatala ndikudwala😅😅 pano tinakwatirana tili ndi ana atatu koma ndikakumbukira ndimadzitsina ndekha mxiiii
2026-11-07 09:19:48
8
Physical therapy :
zomwe anandipanga alamwanu mmmm mpaka panopanndimazuka pakati pausiku kumalira