I wish could I joine CCAP km awa akundifoketsa, tandilimbikiseni a CCAP
2026-10-27 21:01:53
1
Susan Nkhata :
Ife nde tinazoloweratu,
2026-10-27 14:09:51
1
Susan mwanyongo :
uhuuu chonena ndilibe
2026-10-27 11:32:59
0
NAPHI :
ine ndiye mpaka imfa c.c.a.p forever
2026-10-27 20:05:51
1
Tinyade muthali :
a CCAP mlipo apa
2026-10-27 11:26:35
23
Aidah chimwala 🥰💞 :
ife stmaonako vuto Eni akefe ndpo tnazolowelas
2026-10-27 18:23:52
5
Miracle :
kaya lankhurani mulimosemo ine chifukwa chosiila CCAP simnachipezebe
2026-10-27 12:19:42
12
Tawina mandawalatawina73@gmail :
ine nnathawa ku ccap chifukwa Cha zolengeza zofuna ndalama km ntapita mpingo wina ndye unali waung'ono km nnapanga realize kut chilichonse chimafuna nthumba kut mpingo uende,mix nnali nsogoleli ndye I understand better now am back ku ccap, pano ndmapeleka bas
2026-10-27 17:34:37
4
Miracle Makanda vele :
mwasow zoyimba
2026-10-27 15:30:58
6
Mrs mzondo :
Ndi mpingo ulionse osati ku CCAP kokha pano chilichose ndi ndalama kut chiyende zazizi
ine nde proud member wa CCAP koma ase this is true 😩🙌💔they tell us tisonkhe zinthu kuti tikaone abusa like every week kumavaya anthu while some people alibiletu olo mchere in there homes woti ayike ku phala 😩😩it's not fair koma
2026-10-27 16:41:24
2
To see more videos from user @thenzo22, please go to the Tikwm
homepage.