inetu mnali busy kuyang'ana microwave, pamwambapo stove kenako ketro pamwamba pa stove eshiiii mutu wanga oyiwalawu bas pobwera mpesa ndayasamo
2026-10-28 16:51:05
0
James :
koma kut tione kut vuto ndindani pamenepo pakat pamamunayo ndi nkazi koma kumbali yanga ndikuone kut vuto ndi wamamunayo chifukwa amaziwa kut Ali ndi nkazi kale chokapezela kazi wina ndichan
2026-10-28 05:36:31
1
captain :
eish koma anthu muli ndi nthawi iiiiiii
2026-10-28 04:06:28
1
Mwayi Banda :
olakwa ndi amunanu kod nkaziyo akanaziwa bwanji kut Ali ndi nkazi amunawo