@tikufelanji1: nkazi wodula 🤣🤣

TIKUFELANJI
TIKUFELANJI
Open In TikTok:
Region: MW
Friday 30 October 2026 06:13:38 GMT
76901
2404
256
596

Music

Download

Comments

user8539347749256
user8539347749256 :
inu anthu akuzunzika Nazo mmabanjamu zimenezo tisiyeni ife
2026-10-30 13:51:57
0
annet.kamodza
Annet Kamodza :
Atumbuka azanga mli pat ? 😂😂😂😂😂
2026-10-30 09:12:53
45
user5366919928175
Anabeib tyanda💕💓💋 :
so it means atumbukafe ndife odula😂
2026-10-30 16:31:12
1
gloria_kalanje
gloria_kalanje :
zoonadi
2026-10-30 16:25:46
0
user5106847320199
julliet juwah :
ine anapeleka ng'ombe 2 ndi 170 pamwamba 2016
2026-10-30 11:59:06
2
1995frackson
Samson Frackson kaike :
Eish abusawa nde achedwatu ine kuno wanga nde tinangogulirana ka drink ndi ka chips basi zatheka mot pano ayi ndithu tili together 😂😂😂😂😂
2026-10-30 15:45:42
0
telegmail.com3
[email protected] :
that's why sindikupita sanga kubanja🤣🤣🤣
2026-10-30 11:54:30
2
christina.damison
Christina Damison :
ndipo ndiye zoona
2026-10-30 09:41:13
0
ellenwanyeta
ellen Wanyeta :
Alomwe tilipo apa please zongotenganazi zithe kuchilomweko ifeso akazi achilomwe ndi odula kwambiri nafeso tizipasidwa chindapusa
2026-10-30 08:00:39
14
user1281719207020
Tammie 🍒 :
Atonga tili pati,🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳
2026-10-30 11:29:16
7
halimahmamba
Halimah MM :
kodi Adam anapereka ndalama ????
2026-10-30 08:55:53
6
user625546167212
chimae❤️🥰🌹 :
asena ndi atumbuka tikuti zikomo abusaa🤣🤣🤣🤣🤣🤣
2026-10-30 11:26:59
9
user1590542717219
Esther Gondwe :
chifukwachake timatelo ife atumbuka koma amatinyoza 😂😂😂😂😂
2026-10-30 10:09:05
3
user5370200151000
Hellen❤️❤️❤️ :
chitipa ladies where are😂
2026-10-30 14:14:34
1
esnart.grivin
Esnart Grivin :
za ife mmalo mwa atambala adzasinthana baibulo [Heartwarming]
2026-10-30 13:30:48
0
user80465923538477
Highly Favoured 😍 :
Kwathu ku blantyre kulibe zimenezo iyaaa
2026-10-30 13:13:36
0
1992tm0
Tee cakes and deco😘🥰🥰 :
nde mulinkhaza tikuona ife ka salary amawalanda ati ndinalowola hahaha amayake akaatumizra ndrama amwauziratu kuti.osathokoza apongoz anu sakudziwa🤣🤣🤣🤣singachite
2026-10-30 09:49:18
0
patie5857
patie :
Adam anapereka chani chifukwa banja loyamba ndli menelo?
2026-10-30 08:52:59
0
rosemandevu963
rosemandevu963 :
😂😂😂 Ndipo inu zoonadi
2026-10-30 10:41:06
0
moseskawinga82
moseskawinga82 :
khani zakuthela
2026-10-30 13:25:27
0
roseminjolo630
Rosmi28107 :
ndipo inu shaaa ulele bas koma ife alomwa bola tambalaya bas kkkk
2026-10-30 11:44:38
1
nyankho3
nyankho25 :
ndipo asa ndife odula ife
2026-10-30 11:46:42
1
giftsamuelchimphu
Gift Samuel Chimphuli :
asena anzanga mulibwanji ndife odala
2026-10-30 10:15:20
0
nkhoma.naomie3
🌊Naomie🦋Jnr🦋 :
watumbuka mwakhala pati😄
2026-10-30 15:14:57
1
thandizochimkango
Thaxxy ChiLioN :
zaziii
2026-10-30 13:22:21
0
To see more videos from user @tikufelanji1, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About