@ishmaellosani: Anthu amalephera kukuthandiza uli moyo koma ukamwalira amabwera ngati achisoni. #MeetIshmael #Nkhuku #Phunziro #TheExplorer

Ishmael Losani
Ishmael Losani
Open In TikTok:
Region: MW
Sunday 01 November 2026 07:02:20 GMT
347261
21590
491
1319

Music

Download

Comments

charlie.s.makunga
Charlie makunganya :
ndikuikila umbon malem madala anga. continue rest in peace father
2026-11-02 20:35:00
1
user4741405905265
gc beibs :
Amen mphuziro lompambana
2026-11-02 21:34:18
1
caroline.dickman
Caroline Dickman :
ambuye atichitile chifundo izi ndizomwe timachita😳
2026-11-01 11:55:30
49
user800737277467
cute bether :
ndipo zona zake
2026-11-02 18:07:28
1
user81978674172120
Brighton byson :
Ndizoonadi abwez apaziko a amakukonda patender km pamavut amakuthaw 😭😭😭😭😭
2026-11-02 17:14:26
3
chifundomwale829
Mercy chisale :
ambuye yumoziwake ndine ambuye nikhululukileni ine pachilichose chimene 😭😭
2026-11-02 19:32:32
2
user6337739624096
Kelvin :
nkhaniyo ndiyoonad😭😭😭😭ana ziona malemu mayi anga Oliver m'manga 😭😭😭😭😭
2026-11-01 07:54:52
26
peterbandah936
Peter B Bandah :
Ambuye tithandizeni
2026-11-01 18:52:12
3
madalitsosaundi
Madalitso Saundi :
nkhuku inalemba bwanji kalata
2026-11-02 17:34:36
2
user2752132791588
Jamia Ajasi :
ndpo ndkuchitira umbon
2026-11-03 02:06:47
2
elizawayson
eliza :
zoonad
2026-11-02 08:39:13
2
hezalcandy1
Asiya 💞💞💋 :
ndende malemu mayi wanga anaziona izizi mzimu wanu mayi uziwunsabe mumtendere 😭😭
2026-11-01 19:11:49
7
user2311948124055
user2311948124055 :
Zikuchitika zimenezo eee
2026-11-01 20:19:28
4
faithrinembungo84
Catherine Mbungo :
ndazivela chisoni ndiuthenga uwu
2026-11-01 13:30:50
3
fazilah.willes
wisy man :
amen ndi zoonad
2026-11-01 07:41:35
7
lizziechikulamayembe
Lizzie chikulamayembe :
amen ambuye atione
2026-11-01 16:59:40
2
chifundoomari445
chifundoomari445 :
Emen
2026-11-01 09:16:55
6
user65947618196621
isabell kazimilo clerakazimilo :
yyy
2026-11-02 03:49:04
2
user6046387690620
Agnès lukwesa :
next
2026-11-02 05:52:47
1
christinemokesi12
christinemokesi12 :
hui 😂
2026-11-01 19:11:03
1
thandieackim253
thandie :
phunziro labwino end ndatorapa Kathy next
2026-11-01 16:07:24
4
charitymlombe
Charitymlombe2007 :
ndipo mulungu akhululuke Amen tiyeneka kumakondan pamavuto ndi pa tengelele moyo kuthandizana Amen
2026-11-02 15:42:20
2
chikalonda
CHIK∆LOND∆ :
iiiiih koma ase💔💔
2026-11-01 21:08:28
1
mimijade51
Mimijade :
liiiiii ndipo hmmmmm
2026-11-02 05:36:54
1
mwanawamussah
mwana wa mussah🥰 :
zoonad Inu iiiiiiiiii mmmhhh 😭
2026-11-01 18:07:39
2
To see more videos from user @ishmaellosani, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About