@pakayatv: Zaka Passover channel inside Pakaya Tv Talk Show with Blesikwa

Pakaya Tv
Pakaya Tv
Open In TikTok:
Region: MW
Wednesday 04 November 2026 20:54:41 GMT
116269
4625
817
639

Music

Download

Comments

ketulomw
Ketulo jnr 🪖 :
ine mmadabwat mwana wanga zochitika zake ngati zaka🥹💔
2026-11-05 01:56:39
238
madakachepa
Mada kay :
ine azaka kaya bwanji content yawo simandiwaza
2026-11-05 06:00:05
134
deborah.bandah
promise🥰♥️♥️ :
km mwati zakayi si nfiti
2026-11-05 13:04:47
9
martin.kayora
Martin kayora :
cha misala ichi
2026-11-04 20:56:46
83
tarian56
Tarian🇲🇼 :
Ati pamenepo Nde u make it clear😂😂😂
2026-11-04 23:31:41
36
hilda_fashion1
Hilda Fashion :
awa ndiye anapengq sured
2026-11-04 21:47:38
28
giftnedi792
Gift Nedi :
kodi tikalowatonse kumwamba?
2026-11-05 16:02:19
0
joh7627
Kadosh🔥🤍 :
ati you make it clear 😭😂
2026-11-05 03:56:14
14
rythm294
Rythm :
Amadana ndi Zakatu ndi mahule. kudana ndikulangizidwa.
2026-11-05 06:44:04
5
gabrieljosua38
josua :
chilungamo cha munthu akalankhula zimaveka ngati ukudwala mutu waukulú,☺️maka akalankhula ma mistakes
2026-11-05 03:50:30
11
rayart22
Rayart :
nkhani yakeyo ikuonetsa kuti munthuyi ndi woyipa ndithu pamodzi ndi azimayi wo.kuyipa mtima kwambiri.
2026-11-05 04:39:14
9
marianikomedi2
REE NIKOMEDI💞 :
🤣🤣🤣🤣tchito ilipo
2026-11-05 15:54:56
1
user71982078781158
Joshua mwale :
zaka amandiwaza
2026-11-05 15:47:16
0
ishmaelphiri
Ishmael Phiri :
ndichifukwa chake ine ndinamuthangisa mkazi wanga ndi mwana woyamba
2026-11-05 03:47:38
1
user449399390990
9999 :
koma zaka😂😂😂😂😂
2026-11-05 14:59:24
0
charity.mhango7
charity mhango :
koma simisala iyi😅😅😅😅
2026-11-05 14:37:51
0
gama.dzimbiri.bria
Gama dzimbiri brian :
zikuchitika koma kwambiriso
2026-11-05 02:38:27
5
joseph.chisale
JOSEPH.chisale :
Amene amadana ndi PAKAYA TV ndi mfiti😁😁😁ameneyo amatamba😂😂😂😂🤣🤣🤣🤣🤣🤣
2026-11-05 08:58:06
2
gertumoyo
gertumoyo :
Bodza
2026-11-05 04:51:49
1
fox76411
fox 🦊 :
ndiye surname ndiyandani anawo .
2026-11-05 10:15:15
0
sammyndinga
Sammy Ndinga :
abusa amenewo kkkkk
2026-11-05 04:32:45
2
qiniso984
Qiniso984🇲🇼 :
Zaka ukufunika DNA test ndi ana a sister wanga kuno, sindikuwona bwino😳😳
2026-11-05 09:37:52
4
felix.kambazina
Felix Kambazina :
kkkk koma iweyo Zaka ase kkkk
2026-11-05 08:45:13
1
breatmandan
triviavtrevor😘 :
in case ts your first time he is mad
2026-11-05 07:46:12
2
blessings16219
Blessings1 :
😂😂😂 iii inu
2026-11-04 22:16:41
2
To see more videos from user @pakayatv, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About