Ndimafuna ndingodutsa koma ndakanika 🤣 kkk abusa si ose amuna amabisa salary with that little salary we Bughet it together And May that little salary increase Ndipo ichuluke kwa azibambo nose omwe mumawuza salary akazi anu
2026-11-06 08:34:20
2
slla :
mau awa abwerera ine mmm ndmaonjeza😥😥😥amen abusa🙏
2026-11-07 10:59:03
3
Nanthala :
wanga pano adafika i thank God
2026-11-05 18:20:32
4
boss lady :
Amwalire basi tisale azimai tokhatokha mwina tinenepeko