@anniek1996: Tikhala tuphunzitsana ma business ochuluka tiyeni tikhalile limodzi

Anniek1996
Anniek1996
Open In TikTok:
Region: ZA
Friday 06 November 2026 08:32:44 GMT
16214
796
147
134

Music

Download

Comments

mimiee2017
Mimie :
afuna let's team up tidzapite
2026-11-06 10:28:06
14
swtsungie
swtsungie😍😍😍 :
a lilongwe Ali pati timvane🥰
2026-11-06 19:29:23
6
isaactheace0
ISAAC THE ACE :
100lt cooking oil ali pa bwanj m'ma kwacha
2026-11-06 20:38:55
1
ndzukulu.wa.a.kang
ANASUWANDE :
Ine ndimadutsapo popita ku Nampula anthu ambili amaodadi konko
2026-11-06 18:38:23
0
mariamayami8
mariamayami8 :
ndazikonda
2026-11-06 17:06:18
0
memwah2
Memwah :
let me follow you
2026-11-06 17:25:45
0
loveness800
loveness800 :
ine ndufuna ya mafuta ndi flour
2026-11-06 11:22:19
2
lebogang3983
Lebogang 🖤 :
I remember nnanyamuka ndekha from Blantyre to Tete ndekha ndekha anthu akukana kunditenga😂😂
2026-11-06 16:30:36
1
lady.c.beib
Lady Chrii🇲🇼🇿🇦🇨🇦🔥🔥💯 :
Ndipo or mitengo ya zinthu zawo amakuuza ndalama yakwawoyo ndi kukuuzatso makwacha
2026-11-06 16:32:00
1
stevekthomas
Steve K Thomas :
thank you sister
2026-11-06 19:17:53
0
aminamsinji
Abeeti W :
nMulungu wayankhula nawe sis
2026-11-06 19:29:25
0
hajeerahblam981
Her❤️ :
Akufuna tipite ndani ??ine I know language plus Malo ambri
2026-11-06 17:20:00
0
humblequeen1111
humblequeen1111 :
inde ndufuna komwe ndingamawode zovala zashop zotchipa zumagulisidwa mtown mu
2026-11-06 14:07:25
0
nachanga3
nachanga :
kodi ku Villa nsalu zitenje zimapezeke
2026-11-06 11:30:29
0
ellahngwendu
Ellah :
komano ineyo ndimaona ngati kupita ndimuthu oti akukudziwa zimachitilako ubwino cous kuti usithe kwacha kupita ku meticais it's not easy 🙌 anyamata amaba eeee mwina ku villa ko kapena
2026-11-06 18:24:07
0
tama750
Tamandani💐 :
pangani group tipange join
2026-11-06 11:27:40
1
shukulanimpasaley
Shukulani Mpasaleya :
Mami ineyo kumbali ya sparget komaso mafuta kod 400 Sousand ndgathe kuyambila??
2026-11-06 13:58:53
1
user8702245715174
Lipita :
ndalma yoyambila itakhala zingt kut ukaode zinthu kumeneko mam
2026-11-06 11:08:45
1
spiiiie20
@spiiiie2 :
Ali ready tipite
2026-11-06 11:49:52
0
livenessmsosa
livenessmsosa :
Tiyeni tipite nditsagane ndindani ????
2026-11-06 12:56:02
0
tiya.m.chirwa
Tiya M Chirwa :
ugayabe ndi ndi bwanji
2026-11-06 11:20:55
1
anniekalumbi
anniekalumbi :
Ine ndinaoitako ndekha ku villa mulanje
2026-11-06 11:39:15
1
memory.samson3
Memory Samson :
Ine ya mafuta ndi super gt ndi Zina zotelo passport ndili nayo kre
2026-11-06 10:32:41
1
madalosimengwa
Mama sophie :
sister nanga anthu amati pena police ya malawi imavuta pena amatha kukulanda ungatani???
2026-11-06 10:45:00
1
emmapnfzihf
Miss Daniels :
TPT nzingati approximately kupita nkubwela
2026-11-06 10:22:01
0
To see more videos from user @anniek1996, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About