ena akudandaula kut pant yo ndye ngwa ulere? ngat ukuona kut pant yo ndi odula kwambili kusiyana ndi product ungapange yo then it's ok video iyi ikupita kwa amene akufuna kuohuzirapo Lunso lo plus kwa iyeyo akuona kut kukagura kathungo ndikodula kwa iyeyo bola kugula pant yo ndikuzipangira ekha.
A Malawi mavuta ndapanga share video kut tiphuzire then nduguliresoni ma pant 🙄🙄🙄🤣🤣🤣🤣🤣🙌🙌🙌🙌
2026-11-07 07:37:12
2
🩷melisha beb🇲🇼🥰 :
🤣🤣🤣odi ndiyese wanga
2026-11-07 15:50:15
0
peculiar's mum :
vuto ine chipañt ngat chimenecho ndilibe ma G anandilowa
2026-11-07 15:35:50
1
chality chimphepo :
ndikazatopa nayetu
2026-11-07 12:34:53
4
laisa jobe :
ndiye pantyo sitikagula kuti tipange zimenezo
2026-11-07 12:21:17
2
8T33Ñ :
Inetu ndaphunzira.
2026-11-07 11:29:12
1
precessjana :
Ndiy ndikadula ndizival chan
2026-11-07 10:55:29
2
Esnart 💕💚💛💜 :
I can't make it how do you make 😄😃😄
2026-11-07 08:56:43
0
Alinafe zulu :
Zili bh 👍🏿
2026-11-07 12:13:17
1
Aaron :
nice
2026-11-07 10:42:15
2
chimwemwe Nkhwazi :
super
2026-11-07 10:01:04
1
Anne Alone :
okay 🆗👍
2026-11-07 13:28:11
0
Fanny Kapyola :
kkkkkkk
2026-11-07 08:56:47
0
estherkumwenda292 :
follow
2026-11-07 08:02:35
0
Sandrah Mogera :
aaaaaa tikamapangachocho amna samazamagura
2026-11-07 20:19:43
0
grecian saiwa :
meaning aleke kuwala kumusi azivala kumwamba
2026-11-07 19:59:20
0
Joyce Mbewe :
panti wanga ulindi matumba nde matumba akhala pat komaso unadowoka kumbuyo🤣🤣🤣🤣🤣🤣
2026-11-07 15:01:41
0
Flavaful :
basi kumangokhala kudula ma panti
2026-11-07 17:22:58
0
blackgold3203 :
mmene mwayenda scissors mo mudzitanuka mufunikabe binding, mwina amene muli nd makina osokela nzotheka
2026-11-07 11:55:46
1
Natasha :
Asikana apano sangapezeka ndi pant ngat ameneyu ndi mikora sete yokhayokha😜🤪
2026-11-07 14:49:32
0
Eve🌹❤️ :
Koma madziwa dzoti or pant ali okutha amavuta kutaya ndy nditenge pant wabwinobwino apedzekeso zoti wakanika 😏😏