Vuto ndilakuti olo mlankhule mpaka na kutuluka malovu kuti MCP izalowaso m'boma ndikukayika , ubwino wake enafe mpakana pano tikukalamba sinayambe ntaponya vote 😅😅😅😅😅😅😅😅
2026-11-08 20:06:06
0
mdzudzuli Yusufu chidolanthaka :
zoonadi simukunama ndichibwana chibwana
2026-11-08 16:55:27
1
Gerie@1904 :
MCP never again 🙌
2026-11-08 19:56:14
0
magowa83 :
dpp zitsilu za anthu
2026-11-08 05:40:19
5
Olive banda :
Vuto kupha mcp
2026-11-08 05:24:29
0
Gibys :
kwa amene sakuvomeleza ayende nsewu wa Blantyre kupita ku Lilongwe simungapeze chimanga munsewu chikupita chigawo chapakati koma kuchoka ku chigawo chapakati kubwera ku mwera
2026-11-08 07:24:34
4
Vitumbiko Nyirongo :
MCP yakupha
2026-11-08 08:13:25
0
Praise Prince :
Tidadzinyenga ndichala. DPP ndiphala lelileni
2026-11-08 04:11:11
2
nafe🥰 :
Koma kuli vininga
2026-11-08 06:10:24
1
Katukumala Auto Parts :
true
2026-11-08 06:30:32
2
amaayankho1 :
🥰🥰🥰🥰🥰 anthu taleka ulima palibe phindu
2026-11-08 05:12:00
0
Liness Mkuzi :
Tidzalima 2030
2026-11-08 07:05:17
1
khumalo :
Koma ndipo inu zovuta kwambiri
2026-11-08 12:36:59
0
user7928884504241 :
Zoonadi
2026-11-08 10:17:58
0
Bolshevik :
tell dem
2026-11-08 06:07:34
1
Annie Chipokosa :
true
2026-11-08 12:35:59
0
Jimmy Chikalipo :
Dpp yabwera kudzapha dziko guys akadakhala madolo a dpp akadapanikiza ulimi zigawo zonse zimene zimadyetsa dziko koma ai ndithu mbuli zawanthu ngati mumati mcp anthu amadya chitedze muziona chaka chamawa