@msanyamakelvin:

Mr Congress
Mr Congress
Open In TikTok:
Region: MW
Monday 09 November 2026 12:19:38 GMT
7624
172
48
31

Music

Download

Comments

emmanuella0787
Emmanuella :
Andale onse ndiwoyipa amangogwilitsa ntchito anthu osauka iwowo kumalemela
2026-11-10 03:47:04
0
user3886888237788
styn :
Ku Malawi kuliso anthu Ngati awa Ambuye pelekani anthu Ngati awa ochuluka
2026-11-09 21:51:10
0
user13305386396611
user13305386396611 :
god bless you bro wayankhula bwino kwambiri
2026-11-10 03:16:37
0
blessings.mwamsam
Blessings Mwamsambo :
mwene ndinu munthu olimba mtima
2026-11-09 14:26:48
1
user8420842683738
[email protected] :
eeeeeee broooooo ai chabwino
2026-11-09 20:08:25
0
chimzime
Marita mwana wamama omalidza :
ine ndiwa dpp ndipo magadzi anga ndia blue koma walankhula bwino ndipo ulindi nzeru bro
2026-11-09 22:27:39
0
ancientnkhata
Bayethe :
Kuyankhula koma kumeneko
2026-11-09 19:02:52
0
standard.seleman
Standard Seleman :
MCP isadza bweleso
2026-11-09 14:13:14
3
jumasize
Jumasize :
grezeda akuva koma?
2026-11-09 16:48:08
1
tsunganani
Sungah Thomas :
ichichi chidyera speech iyiyi
2026-11-10 04:14:31
0
user4631652716715
user4631652716715 :
aunze
2026-11-10 03:48:12
0
fundo527
#fundo$ :
kuyakhura Koma kumeneku ine ndiwa DPP Koma ndadzikonda
2026-11-09 20:15:37
0
precious.banda973
Precious Banda :
mawu amenewo bwana kuyankhula koma kumeneko mkabwela kwa msundwe mdzakuwoneni mwatiyimila tonse a MCP
2026-11-09 18:19:41
0
blacky.b.malunga
BLACKY B Malunga :
kuntchaya kugwetsa comrade mwatiyakhulira amalawi achinyamata ambiri ndipo osati mcp yokha kma zipani zonse
2026-11-09 18:27:34
0
basheell
user23927632650435 :
Ndazikonda kwambili I'm from mangochi
2026-11-09 17:59:32
0
rashastingschikafanyomby
RAS HASTINGS NYOMBY DIHDIH :
thats the kinda youths we want as a a countty.
2026-11-09 17:50:37
0
142escobar2
A.T.kalibwanj :
not mcp supporter but this is the way to go kuyakhula osaopa
2026-11-09 13:35:56
0
rhodrickchinkhali4
C G D :
kuyankhula kwa nzeru koma uku
2026-11-09 14:27:06
0
user9923186240515
user9923186240515 :
kkkkkkkkk[Laugh approved][Laugh approved][Laugh approved]
2026-11-09 13:48:47
0
armitagehardson
Armitage Hardson :
kkkkkkkkk
2026-11-09 14:16:56
0
zumarichard
JUMA RICHARD :
point
2026-11-09 18:17:44
0
lloydmkula
Manda aliza :
anyamata azilimba mtima
2026-11-09 14:12:51
0
sambo.wa.sambo
sambo wa sambo :
kuzolowela zaulele achingwa ntola
2026-11-09 14:35:15
1
johnstone.mngomba
NACHIYE HILLS INVESTMENTS.JMB :
Chakwera anali wabwino kwmbr ndipo zitukuko zinali palipose. vuto lomwe linapangitsa kuchotsedwa m'boma munataya makiyi pa CHILIMA,posalemekeza mgwirizano wa TONSE ALLIANCE kulitenge dziko lopusa agreements kupanga ku institute kma pambuyo ndikumakana. eeeeeeshhhh dziko linakwiya kwmbr R.I.P. SKC next osadzapangaso kulemekeza agreement basi
2026-11-09 21:13:28
0
user2129816808838
Tonny .T. Andy :
kuswa kuswa 🤣🤣😅
2026-11-10 00:44:08
0
To see more videos from user @msanyamakelvin, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About