@user5237932498199:

KEN NGOMA
KEN NGOMA
Open In TikTok:
Region: MW
Tuesday 10 November 2026 15:10:15 GMT
37885
1579
340
281

Music

Download

Comments

patrickesaukamang
professor Kamanga :
chakwela my presdent ndalama zimapezeka. buzness imatheka koma pano buzness sikutheka anthu alibe ndalama. nthawi yachakwela kugulisa thumba limozi la soya umakwanisa kugula thumba la fertilizer pano ayii ndithu tikanika kulima. chakwela ndi dolo nsaname ziko lanukha. ilii
2026-11-11 11:32:25
1
mondwe1999
Emmanuel mondwe :
ndimanenatu nthaw zambiri kut dpp sisamala moyo wanthu koma kusamala zamabanja awo
2026-11-11 03:57:27
11
matabbie4
matabbie4 :
ndipo chakwera sangakhale mfumu koz even kumwamba kunamukama
2026-11-10 19:56:51
2
dolisagondwe8
Priscilla munthali :
ineso unditenge ndikapepese nawo
2026-11-11 19:25:37
1
charles.mkonkholo4
Charles Mkonkholo :
ka ndalama kamawoneka nthawi yawo
2026-11-11 17:57:40
6
user84501557861955
Bryan :
ndipo ndalila ine😭😭 kuwasowa achakwera
2026-11-11 19:20:30
2
giftmhone421
Gift MHONIE :
chimaonekA chakuya chikaphwa🥰🥰🥰🥰🥰🥰🥰🥰🥰
2026-11-10 21:14:53
8
ruthkambaye8
Queen Ruth :
ndipo ave kupepesa ishiii 🙆
2026-11-10 18:50:50
11
lizzie.msonthi
Lizzie Msonthi :
ineso ndipite nawo
2026-11-11 13:39:54
1
alice.chanza
Alice Chanza :
ine chakwela yekhayo nde ayi bola kabambe
2026-11-11 14:35:00
2
patrica19545
Patricia Richard :
ulemu upite kwachakwela
2026-11-11 09:46:19
1
mikh.com005
Mikhateees :
Ndimangova zogona pamafuta Pano ndiri pamenepo Koma ndiudzudzu wanji? Chakwera nkhululukanI Baba siziri bwino tifatu ana anu
2026-11-10 19:30:22
11
user3004408777132
Mdiwas :
nde mwati tilima koma
2026-11-11 02:01:54
5
user74569165699761
humphreys kwachakale :
Amen and amen tikhululukilen achakwera
2026-11-11 11:18:32
1
alicechakwana979
Alice Chakwana :
km ndiye zinthu sizilibwino ai aaa ndipo amene angayamikile a dpp ameneyo amadya manyi ake omwe sure
2026-11-11 02:54:13
5
user8376017739750
De Boy :
ku mcp kulibe okutha kuimba ndaonera apapa
2026-11-11 07:35:04
1
ulemumasamba355
Ulemu Masamba :
zaziiii mwana nyimbo
2026-11-11 03:53:03
1
facenessmaneasy
Faceness maneasy :
amalawi tinapanga mistake
2026-11-11 19:00:23
4
matabbie4
matabbie4 :
Hahaha 😆 😂 😆 pitani ukawapepese ine sindingapepese chikangawa
2026-11-10 19:56:21
2
olivetakampira
olivetakampira :
Aaaaa osayimba yanu bwanji
2026-11-11 15:54:54
0
grecemathew
grace :
ndiwathu ameneo 2030 boma
2026-11-11 18:25:11
2
chimwemwe029
Chimwemwe :
100% correct apepesedwe a pure
2026-11-11 08:28:50
2
aliciamundie
❤️Nikhiwe 🥰 :
atikhululukire anthu ambiri anamwa mowa pa 16 SEP 2025
2026-11-11 09:51:37
3
fynesschakhumbira
Fyness Chakhumbira :
kkkkkk amalawi ambiri mudaledzeradi pa 16 sept .ambuye akukhululukireni sure.
2026-11-11 13:18:24
3
user118419688851
Mercy wa Banda :
Mmm yasinthaso nyimbo ija abale kkkk
2026-11-10 18:29:29
0
To see more videos from user @user5237932498199, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About