@damianoenoque:

D.Siquelo
D.Siquelo
Open In TikTok:
Region: MZ
Friday 13 November 2026 11:00:58 GMT
95138
2298
1031
1032

Music

Download

Comments

lytonbanda882
lyton banda :
ndy ndalana imodziyo ili nd vuto lanji kuti ikagwilizane ndi kutha kwa dziko , ndichotseni umbuli
2026-11-15 06:37:38
0
fundowabornkhwakhwa
fundokhwakhwa :
owelenga khala Maso nthawi yatha🙌😭😭😭😭😭😭
2026-11-14 05:35:19
0
amandakora5
kora * :
koma zugwilizana bwanji ndi kubwela yesu🤣🤣 koma umbuli sizithu
2026-11-14 04:13:24
37
sparkle.lusungu.k
Sparkle Lusungu Kisa :
Those who are awake akudziwa chomwe chikuchitika
2026-11-14 04:54:54
71
tapiwa6300
tapiwa :
Bible silinama
2026-11-13 18:16:34
115
mphatsobanda2252
mpha :
mipesa izanga sizachilendo iz tinapangapo ma bible study okhudza ndiizi et owelenga akhale mmaso
2026-11-14 04:53:01
25
grace.zachariah8
Grace Zachariah :
Bible silinanapo abale nthawi yake basi
2026-11-14 12:24:18
2
kasanga075
Luna :
Tinkangomva tili ana lero ndiizi
2026-11-14 14:57:36
2
ketrina.kaunda
Ketrina Kaunda :
sikuti ndi president ai koma nthawi ndi imene yathadi malemba akukwanilitsidwa tikufunika kuzikozekeletsa ndithu
2026-11-13 18:23:03
45
preciouschitsa448
hate hate :
Ku Europe amauser ndlama imodz same as Ku America nde litha pot ife tikufuna ndlama imodz?
2026-11-13 20:47:02
29
user6222411314057moree
Liah :
666 yayamba ikatelo
2026-11-14 11:16:30
7
manziehunter
Manzie :
😅😂🤣😂😅🤣using a single currency is good
2026-11-14 02:23:17
8
sarahsa307
sarah :
Kod nde kut zimakwanilisidwa mzoipa zokhazokha? Mulungu amatikonda tonse ndipo ine ndufuna yesu abwere dziko lithe ili tikaoume linayamba ndi kale tione zina
2026-11-14 12:49:00
6
user2555549339274
Hopeson nyirenda :
Izizi nde nd zabwino kwambiri sisatanaso ai km zinthu zisintha kumenek
2026-11-13 18:20:19
11
user8000377818234
Sandra Kumwenda :
osamaphatikiza nkhani ,Kodi mukapita kunja kukaoda zinthu mumauser Malawi kwacha??ndiye chavuta chani Ku ma user dollar?nthawi yatha kuti aaaaaaa
2026-11-14 04:19:55
6
rainfordmalembo
captain malembo :
Jesus is
2026-11-13 20:29:04
16
berthamathanda836
favour jb :
666 apa ndye yafka sopano yesu akubwera bs ,
2026-11-14 00:16:30
16
sheaffermuva
sheaffermuva :
better chakwera
2026-11-13 17:17:32
6
bamboanuopeza
Bambo Anu Opeza :
Yesu sakubwera pano ali busy
2026-11-14 04:09:55
18
charity.katenthe
Charity Katenthe :
amene amawelenga izi akuzivetsa ndipo akudziwa komwe likupita,amene mukuti dollar imagwilitsidwa maiko angati tikujunvetsani popeza masiku akusadziwa Mulungu analekelela. Owelengawe khala maso,nthawi yatha
2026-11-14 04:08:39
13
wexy320
Nuellah🥰 :
munthu osaziwa malemba akuona ngati izi it's simple but those who and understand the word Azindizikila malemba akukwanilisidwa
2026-11-14 15:27:51
5
trynesskasimba
Tryness Zgambo :
mmmmmmm nthawi yoti ana a mulungu azuzike yakwana
2026-11-13 19:44:17
19
user2930811091614
Nawera :
JESUS is coming soon repent
2026-11-13 17:34:49
12
phadyxephiri
Phadyx E Phiri :
Zimenezo ndie zizindikiro Za masiku otsiriza yesu ali pafupi kubwera bac
2026-11-13 19:41:02
7
eunicewatson853
eunicewatson853 :
nthawi yamapeto idzankhala yowawitsa kwambiri kukubwelaku moyo uzalimba, tizikozekeretse moyo wathu.
2026-11-13 17:52:56
5
To see more videos from user @damianoenoque, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About