ma agent azanga osaopa 😂😂😂 your money your rules 😂😂 ma customer ena ngochimwitsa
2026-11-14 04:00:14
12
Mada :
ndipo muli kuyankha mwano
2026-11-17 06:52:00
1
fumercie :
at first ndinkaona ngati ma agent ndioipa until I start ndikuona kuti customer akufuna kutimiza ndalama koma number sakuziwa koma iweyo process wayamba kale 😂😂😂 proudly agent
2026-11-13 15:32:02
15
Martha Chawinga :
At last thank you
2026-11-17 07:12:12
1
Clara Kamaliza :
nkhululukani ndithu akasi😂😂😂
2026-11-17 07:27:56
1
Fu-nda-ll ❤️ :
Agent wapa hardware mulibe anandiyankha ntamufunsa kuti nditha kutenga ndalama ku airtel money? Ali sindimayankha funso limenelo. Pompo ndimangomudutsa mpaka pano😂😂😂😂😂
2026-11-14 05:30:12
6
😊😊😊 :
amayi apa queens mpaka nnapamga cancel transaction kuyakha ngati ndalozesa mufti
2026-11-13 13:58:43
25
Angie beib :
AZIMA APA GATE YA SHOPRITE chichiri ngt ndiwatukwanetuu,Mulungu aziwalangaa😂
2026-11-13 14:54:18
64
DICKIEZ 🤴🇲🇼 :
Kuzimva ngati bank ndi yawo 🤣
2026-11-14 03:22:23
29
Jessica katema :
😂😂😂😂😂😂 ndpo wina alipa ginnery corner pa standard bank
2026-11-13 13:47:29
80
Lusiya :
mwandi sangalasatu chimwene
2026-11-14 09:00:21
5
The style Cart🛍🛒 :
Nde amakhala ndima mood ngat mwayambana
2026-11-13 16:02:07
28
Esther Erick :
ntchito ija ndyotopesa
2026-11-13 17:32:50
8
Letina Mcpetrol :
😂😂😂azanga airtel money chonde tiyeni tikhale ndi ulemu tiziwalandila bwino ma customer mutinyozetsa enafe ku school tinapita koma tchito ikutisowa 😭😭😭
2026-11-13 16:06:21
7
To see more videos from user @msenaosamba, please go to the Tikwm
homepage.