ineyo ndifuseko sindikupanga period chichilireni mwana pano chaka ndi mwez
2026-11-16 19:08:42
7
promise m nyika :
ine sndkupanga period
2026-11-16 20:23:28
0
Dennis💦 debbies💕💐💟 :
amene tili south tingakayezese kt tiziwe ngat tili safe
2026-11-16 12:58:57
12
groria banda :
ine ndmamva kupweteka mbali imodz ndchan?
2026-11-16 07:02:42
10
Doreen zam,mimba :
zikomo kwambiri mama tikatenga
2026-11-18 17:22:04
0
Tiyamike Gondwe :
matenda oipa kwambili amenewa koma zikomo uthenga yamva mama
2026-11-18 14:59:19
0
ivy :
Ine ndiye after 2 years ndimakayezesa apa ndinayezesa January chaka chino anandiuza kut ndizapitenso 2028
2026-11-18 18:32:28
0
tadalachilunjika :
zikomo yaphunzira km ineyo ndikumamva pen pa nchombopa km
2026-11-18 12:57:26
1
Mayamiko Ngozo :
ineyo ndikamagona ndi mamuna magazi amatuluka koma pena ayi
2026-11-17 04:39:37
1
Lau :
ku Lilongwe amaeza kutiko?
2026-11-16 15:47:26
1
tama :
kma ine ndimangopanga period mosarekeza
2026-11-16 10:43:06
1
JUSTICE CHAVULA :
number mbwani cct
2026-11-18 11:18:35
0
Ratifah :
ine mwana wanga ali ndi 1 years km period mwezi uno wachiwili sikusiya km sinditenga kulera aliyese
2026-11-17 22:20:33
1
Everly msachi :
ineyo ndika choka kupiriyodi timaturuka tizironda kumaro obisika nina pita ķuchipatara koma ninawa fotokoze koma bare chomwe anandi uzapo nde chonde chingakhare chani ndithandizeni
2026-11-16 14:18:09
1
Mwayi🥰😍🤩 :
Mai anga anamwalira ndi cervical cancer yomweyi 2018 pano chomwe namphinzira ndukayezetsa anandipatsa 3 years
2026-11-16 15:59:41
3
thokozilegama633 :
@[Pray][Pray][Pray][Pray]
2026-11-18 18:25:30
0
Mimi :
Thank you for this beautiful and insightful information
2026-11-18 10:18:08
2
Meme :
ineso sindikupanga period koma kurerra ndinasiya now three months have past offcous ndiinadzakhala ngat ndayamba period kma kkapangidwe kake mmm sizimandidarutsa ayi kufikiras mwezi unowu ndinangoyamba for one day ndikusiya after some days ndinangoonaso magazi pang'ono doo ndikusoya ndie ndingat imeneyoi ndi period momwe zimakhalira azimayi anzanga mukasiya kurera kut period imabbeera choncho? inde nsana nawo umandivuta ndinkat ndikurerayo akundipangisa koma ndikumadabwa kuti zakurerra ndinasiya koma nsana ukumandivutabe
2026-11-17 21:43:49
2
Priscilla M'biza :
zikomo kwambiri mama mukumatitsekula maso kwambiri
2026-11-16 12:04:12
7
Chrisean :
zikomo kwambili doctor
2026-11-16 17:35:03
0
Aisha Danger :
nanga ngat ukufuna akazi onukha ndi chani
2026-11-16 09:06:09
2
Juriet Chisale :
amen zamveka koma ife tir ku south Africa koyezako tingapite kut a nurse
2026-11-17 06:43:04
0
Nancy Alli :
zikomo adotolo mwatithandiza,mnaluza mayi anga ine ndi vuto lomweli,mmadandawula mpaka pano.
2026-11-16 17:17:02
1
Mable Ngwenyama :
Zikomo kwambili km ine mauka akundisausa eeee
2026-11-16 10:09:55
0
H.M Fabric centre :
kod munthu amene anachosedwa ovary imoz angazakhaleso nd mwana??
2026-11-16 12:19:23
1
To see more videos from user @banda97000, please go to the Tikwm
homepage.