@ztvchannelpoc:

ZTV Channel POC
ZTV Channel POC
Open In TikTok:
Region: MW
Thursday 19 November 2026 16:38:18 GMT
27069
1674
533
103

Music

Download

Comments

haswell.malingamoy
Haswell malingamoyo no1 :
vuto ndiloti amalawi amalemekeza makape promise alibe chilichose iweso zaka ukamati promise ndi bwana ndiweso kape chifukwa dzovala si kulemela wava
2026-11-22 03:55:49
2
terry.ruthson.kat
Terry Ruthson Ras :
A promise ndachimidzi inu aaaaah 😂😂😂✌️
2026-11-20 06:06:29
31
ellen.kenneth7
Ellen Kenneth :
Kaya mutinena kuti ndife asanje koma promise waonjedza
2026-11-20 08:30:05
31
fortunebeib2
FOR🥰💚TUNE🍇🍏 :
lnuso muzikhara ndi limit poyakhura bambo lnu
2026-11-20 13:24:22
16
anita.kayenda5
Anita kayenda :
Azaka musamude pro l love promise
2026-11-19 20:20:13
9
chisale290
chisale 2020 :
ndipo promise amandibowa kuzitamandila ngat zimai
2026-11-19 19:51:43
45
millycent201520
Millycent Nyabotha :
Kaya mundinena koma Primise nasandiwazepo pa page pake palibe chiphuzitso kwa ine Kaya fukwa cha umphawi wanga
2026-11-20 11:29:57
10
lukachakokomamwan
Luka Chakokoma Mwanza :
ndee mwati mukanyenga mfumu?🤣🤣🤣🤣Kudzulaaaaa
2026-11-20 05:07:05
7
esaumalonda
Esau Malonda :
promise ndi kape amuna sitimufira
2026-11-20 03:51:09
12
paulkasongo681
paultembo :
ndipo ine promise amandinyasa mwayakura bwino madala.
2026-11-20 00:25:27
23
user6928820776759
Coshaki :
kaya ndiye ndikuseka chani kaya
2026-11-21 18:12:13
2
emmanuel.abdula.s
Emmanuel Abdula Sano :
ndikape promise kuli azake komweko koma sazipopa kod Amaona ngati aliyese alibe kuthekela?
2026-11-20 04:50:17
12
he_is_placid1
HE IS PLACID🔥🙏🥹🌏🖇 :
Ndikudzule ndisakudzule?
2026-11-21 01:44:44
6
malawitv2
MALAWI TV :
Ati ukhoza Kupanga Stroke, 😂🙌
2026-11-21 22:48:06
1
user2296304027194
user2296304027194 :
promise amadziva kwambr ndiye mulungu amatsitsa odzikwezatu end bola anakamatcuka kuthandiza ovutika kumalawi kuno
2026-11-20 05:09:27
9
luciabandawe
Lucia :
zilungamo zokhazokha
2026-11-21 11:48:25
1
user16667945024774
polinakatawala6@com :
live zaka
2026-11-21 19:01:25
1
gracekameme2
🌸GRACEFUL GEM💕💕💕 :
🤣🤣🤣🤣🤣 koma ndaseka
2026-11-20 07:22:39
6
fracksonnkhoma928
Joe👑 :
Wamuchita bwino ndi opusa Promise
2026-11-19 20:30:08
9
cristalwest41
Musa Chingawe :
Passover channel ndi zaka mulibwanji
2026-11-20 01:15:43
5
queen.baby1677
Queen baby🥰🥰 :
😂
2026-11-21 07:27:15
1
user2159010511360
ellena :
kmd mulungu anatibisira zamawa
2026-11-21 16:46:31
1
mrscreenshot1
Jeff Chw198 🇻🇳🇨🇳🇲🇼 :
Mayi ake a promise mwati Anyengedwa b4 December 😂🤣😂😂😂
2026-11-21 13:57:42
3
haswell.malingamoy
Haswell malingamoyo no1 :
komaso kodi kulemela kwanji konjabula sapato ndalama alibe uyu matama chabe atiwonetse zithu zenizeni osati dzovala
2026-11-22 03:51:31
2
To see more videos from user @ztvchannelpoc, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About