@tikos_englishfy_chichewa: #englishlearning #Mbandira #technicaltraining

Tikos wa Englishfy Chichewa
Tikos wa Englishfy Chichewa
Open In TikTok:
Region: MW
Friday 20 November 2026 09:54:00 GMT
17250
834
95
176

Music

Download

Comments

mercywellengu
Mercy Wellengu :
zophiiika yekha mwana zopatsa busy
2026-11-21 03:14:15
0
saujatichiunga
Gloria Chunga mustafa :
Chonde can help me your way number please
2026-11-20 18:13:53
0
afshaqassim
Afsha Qassim :
Ndikufuna kutimiza mwana wanga insha'Allah koma ndizambiri zomwe ndikufuna kudziwa ndingakuyankhuleni pa # mwatumizao
2026-11-21 11:03:00
0
emmied48
aaaah :
ndakonda kuzapanga nawo ntchito zamanja chidwi ndilinacho koma mapezedwe andalama kwathu nzovuta ...ndimakhulupira KT mulungu azandiyankha zofuna zanga
2026-11-20 11:22:36
5
chrimemo2
Chrimemo :
Ndazikonda
2026-11-21 07:54:57
0
khwima.chawa
Khwima Chawa :
kunkhwotatoko ndidela lit ndizatumizeko mwana wanga
2026-11-21 09:48:21
0
eunice.mlumbe.phi
Eunni🥰❤️🥰❤️❤️❤️❤️❤️❤️ :
muli ndi Malo ogona oti anthu akutali azizagona konko?
2026-11-20 19:20:55
1
user9154521861076
chikwanje :
kwatalika kuchoka ku thyolo
2026-11-20 17:01:10
0
rhodaissa
rhodaissa :
palibe ya online ndili kutali ndimafuna certificate yo ine ndili serious
2026-11-20 13:49:54
0
saidichalemba2
Saidi Chalemba :
Kodi electrical installation sitheka online???
2026-11-20 14:50:50
0
chiperxyvendors
Dorophy :
Taikani phone number yanu tilankhule nanu plz
2026-11-20 18:02:18
0
wysonseven0
wysonseven :
Koma zili bwino
2026-11-20 11:07:52
0
violetbanda808
Violet🤍😘 :
interested
2026-11-21 08:53:48
0
princelbadna12
PRINCE BANDA :
nkhotakota mbali yapatipat chifukwa ineyo ndili ku Dwangwa komano ndikufunakut kupite mung'onowanga komano nkhan yachakudya bwezi mutayikaso kut tizingowelengesa zonse pakaumodzi
2026-11-20 18:16:55
1
medschimera
Meds Chimera :
your number sir
2026-11-20 18:24:46
0
benjamin.rodgers2
Benjamin Luhana :
tumizan nambara please
2026-11-20 22:44:08
0
user5704614306513
shalom :
ponyani # yoo chonde
2026-11-20 21:35:28
0
agness5315
agness :
ambandira ndimafuna ntamumumidza mwana wanga koma zophika yekhazo mm
2026-11-20 11:10:05
0
eunice.mlumbe.phi
Eunni🥰❤️🥰❤️❤️❤️❤️❤️❤️ :
o
2026-11-20 19:21:17
1
elizabethn505
Elbeth🥰 :
kwangonditalikira
2026-11-20 13:07:55
2
meria7334
meria :
akutali amagonela konko ndili ndi mwana wanga wa form 1 koma sizikuyenda
2026-11-20 20:04:20
1
tenniswadi
Tennis CEO :
This is great thing ever
2026-11-20 16:46:37
1
favourchimangeni
favourchimangeni :
kwangotalika koma
2026-11-21 08:21:43
0
user6697462270905
matrida mwale :
ndimutumize phwanga ine
2026-11-21 08:14:41
0
malala.cos
Malala Cos :
nxt year Mwana wanga kungolemba 4 akubwera konko
2026-11-21 09:05:17
0
To see more videos from user @tikos_englishfy_chichewa, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About