@maxandsherry: We showed up m’mudzi wa Matale ku Ntcheu for this woman. Her story is a life changing encounter! In the 1980s and 1990s anagula malo oti panali kasupe, madzi samasiya kutuluka mu nthaka throughout the seasons. Kunali ku Naperi mu Blantyre. Anthu ovutika ambiri amene sankakwanitsa madzi a waterboard ankawalora kutunga kwawoko mwa ulele. Analinso ndi chipatala, ankalora anthu osauka kuthandizika mwa ulele. Family imodzi yomwe inapangako benefit inali ya a Norman. Mwana wawo wa a Norman, Ulemu, anali chabe ku Primary School koma she remembers vividly every detail of her kindness. Now mai and bambo Norman are long gone but their daughter has not forgotten the kindness. Lero she is in the US and she says,”moyo wathu sukanakhala pamene ulipa chipanda amayi awawa, mupite mukawafufuze komwe ali mukawapatse K2.5million”. The good and the bad will do will always live after us! God bless grateful hearts! This, too, is love❤️🙏
Max-and-Sherry-Dine-and-Lounge
Region: MW
Saturday 21 November 2026 21:33:34 GMT
Music
Download
Comments
vero WA izack :
mukafika ku lilongwe munene Pali banja linalake linandipanga khaza kwambil thaw yomwe ndimakhara pakhomo pawo Koma khaza zawo zinandiphuzitsa kulimba ntima kudzalila pandekha popanda khazazawo bwezi ntakula mopusa mukawayamikile plz mukadzabwera kulilongwe mudzanene🙏
2026-11-22 04:15:41
49
GraeCieeh :
Dear God,is this how you work?????
I can tell this is a miracle to her
then Ambuye ineyo ndidikila ,,,,,,,,,
God bless this Woman and may she live long
God bless the Menzuwa's momwe mumaperekela uthenga mmmm so interesting, talira nao😭
And God bless the one who have remembered our Granny, it's not easy
Kuyamika ndi kwabwino pa zomwe Ena anakuchitila
2026-11-23 18:30:30
1
DM :
Hope, Mwawapeza kuti Amayi anga awa. Mai Gwizima. She's the only one who could decorate freely kudya Entertainment center Hall during the early years of my Preaching Ministry. Amayi awa and her husband did alot of good for me and my Ministry. Hope, Help me to meet her ndiiithu.
2026-11-22 06:01:05
50
nanabello :
late Brian Banda ankanena nthawi zonse kuti kumakhala bwino ndi anthu Mulungu anatibisila mawa
2026-11-22 04:12:29
102
wayne265 :
ndalira nao nawo ine
2026-11-22 05:13:45
58
Angella Sandra :
Koma Tamika ndiwaulemu eeee,,
2026-11-21 22:05:05
61
Shaloh97 :
When she knelt down oooh dear God this woman trust you..🙌🙌
2026-11-22 07:18:11
40
Ku Makata🧺🇲🇼 :
For Max & Sherry - This is a calling from God[Fire][Fire][Fire][Fire][Fire][Fire] You can even fill the anointing in the narration of the story!!!! Like he was there in those years… he made us imagine it.. is it just me ? I visioned the whole story as he was speaking……. This is not just a business for you , but a business God put on your heart, you are living your purpose!!!! Don’t stop!!!!!!!!!!
2026-11-22 15:38:02
17
Thecrossacademy :
Agogo mwandiriza Sunday morning. Mwana amene wapereka mphatso iyi ambuye apitirize kumudalitsa. Kumathokoza munthu akatichitira zabwino.🙏
2026-11-22 04:49:19
44
E🫧🪷 :
Amachita kundiuza ine ndili mwana madzi akasiya kuti Ellah bwera uzatunge usayime pa nzele 🙌🏻🙌🏻 if she didn’t mention her name I would not have recognized her I was young. But she is an angel 😇
2026-11-22 11:40:55
30
Curio seraph 😎 :
:have you notice kt ndalamayo akufuna amangirenso church mmmh Mulungu aziyadalitsa kwambiri🥺🥳
2026-11-22 07:46:44
23
Mpendadzuwa :
Awwwwww God bless her. It’s beautiful to see her honored in the land of the living
2026-11-22 17:58:11
0
Cha~ris :
Jokes on you , I was planning to cry today anyways 😭😭😭
2026-11-22 10:54:20
23
Jay :
you can even tell that Agogowa is a very kind lady, zosangalatsa izi
2026-11-21 22:32:26
20
Chris🇲🇼 🇮🇱 :
This is the only prayer that works
2026-11-22 10:31:53
15
nacymas :
Ine ndalira nawo 😭
2026-11-24 08:31:06
0
Annia❤️💕💞 :
ine ndingolira😭😭
2026-11-24 11:13:27
0
Agnes Mandalazi :
amen agogo
2026-11-22 21:31:44
1
Charles Ngotima :
the message we need on social media .. very educative and very powerful .
2026-11-22 04:44:49
24
Nessa24 :
Such a beautiful kind old lady🥰🥰🥰🥰🥰 mulungu mulemekezeke
2026-11-22 02:59:38
26
Felix William :
mulungu anatibisira mawa lanthu
2026-11-22 10:33:06
10
MsLue :
Another day crying on this app, she's a wonderful lady
2026-11-22 06:06:05
17
Joanbellings :
Awww😭❤️she is such a beautiful soul!
2026-11-22 04:17:41
15
young investor 🇲🇼🇹🇿 :
ambuye asungeni agogo anga ndi moyo tsikulina dzapange surprise she means a lot that woman
2026-11-22 04:47:25
16
Tiyanna :
kulidi mulungu kunjaku❤️🥰
2026-11-22 04:39:06
14
To see more videos from user @maxandsherry, please go to the Tikwm
homepage.