@kasenyatambala:

KASENYA TAMBALA
KASENYA TAMBALA
Open In TikTok:
Region: MW
Sunday 22 November 2026 09:49:09 GMT
88784
5296
374
1132

Music

Download

Comments

ndinevai
Ndine Vai :
Ife za afitizo ayi Koma tatithandizeni za mmene tingathane ndi mbava zotchola nyumba abale ...andilangaso😭😭
2026-11-24 19:57:40
4
akimunyirenda
Akimu Nyirenda :
Nde inuyo munaphunzira kuti komaso mumaphindulanji pa zaufiti or amaphindulanji afiti, ine chomwe ndidziwa or ukhale ndimankhwala azisamba ambiri bwanji koma tonse siku lizafika lomwalira just kutaya nthawi
2026-11-22 12:00:05
9
priscillamangata2
Priscilla mangata :
nyumba yanga ilindimakomo atatu ndiye ndipanga khomo lake litilo
2026-11-22 20:37:35
6
selina.zonga
Selina zonga :
give me my number my brother
2026-11-23 06:25:25
4
zahidahmchipember
ZahidahAlicia :
Koma mesa ndinava Kuti fiti silowela pakhomo imalowela pakhoma ndye ngat sadusapo pamenepo
2026-11-28 08:13:37
1
musician.raph.k
artist Raphael kumwenda :
koma makhwalawo sakukwana ine makhwala ndimawaziwa koma zila ndisingano palibe chochitta palimitengo apo mwav kwalimwe salu yapiliod koma kunenako mmmmmm
2026-11-23 07:33:49
3
osamba58
Riziq :
ndinali ndi mwayi linaphulika nyumba ine ndili panja
2026-11-27 22:29:14
0
judithchikadza
Mrs Vascocellous Manuel ❤️ :
tili pa rent tu
2026-11-22 20:30:52
3
pemphero.golden
Pemphero Golden :
mumakwana big
2026-11-27 20:41:59
0
tensonkamasisi
tensonkamasisi :
Big man 🙏
2026-11-28 04:53:21
0
cynthia.lyson
Becky :
zamveka mwene
2026-11-27 05:48:16
0
alicemukuka44
Alice mukuka :
thanks
2026-11-28 15:44:09
0
jane.beab2
Jane beab :
ife tili ku jonife tingapangeso
2026-11-22 12:42:28
1
thyela.simba
thyela.simba :
Nanga kwa eliya?
2026-11-23 17:40:26
0
yamikanichikaonek
Yamzy Military :
Majority pa Malawi pano ikukhala pa rent nde iwe monga landlord ukapeze tenant wakumba panyumbapo unva bwanji???
2026-11-25 17:50:15
0
user4216107372378
carlorine :
Ineso ndipanga
2026-11-23 13:16:53
1
salika.daood
Salika Daood :
Ifeyo timapita kwa Mulungu basi
2026-11-26 09:29:20
1
1994cuteolie
call me mama olie🥰🥰❤️❤️ :
tsono pa rent tipangeso?
2026-11-23 17:37:18
2
groliabonomal
Grolia :
Abale ife nde tilipa rent
2026-11-24 04:03:17
1
mercy.mithi7
mercy mithi :
zkomo kwambir mwatithandiza anthuwa akuwonjeza
2026-11-25 14:24:58
1
marybrucn94
Mary banda :
ikani mulungu pasogolo
2026-11-24 19:57:01
1
omzyymw
Omzyy Mw :
afiti akuvanawo asitha stail
2026-11-26 20:40:38
1
user372926471
user372926471 :
Number please tilankhulane malume
2026-11-24 13:14:53
1
grace.beib.mercy
grace beib mercy 🥰🥰🥰 :
ife tili pa lent
2026-11-23 08:08:04
2
chimwemwemhoni
tha gilr feli :
nde ndingaziwe bwanji kt apa tapeza sing'anga wabwino tithandizeni coz munthu ine ondironda achuluka apite basi
2026-11-23 16:14:48
2
To see more videos from user @kasenyatambala, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About