@imyvoicemalawi: #Ivoicemalawi #malawi #malawiticktocker🇲🇼 #followers

I VOICE MALAWI 🇲🇼
I VOICE MALAWI 🇲🇼
Open In TikTok:
Region: ZA
Monday 23 November 2026 10:27:15 GMT
350
26
5
0

Music

Download

Comments

go.deeper22
Go Deeper :
sindimaiwala malo amenewa ndinabwelera dzenje lokumbakumba atandiwombera chipolopolo kundiwombera mmimba kuzatulukira kubhibhila malo awa 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
2026-11-23 11:19:04
0
daphdz0
Daphdz :
Phillip🙌🙌🙌🙌🙌
2026-11-23 11:36:20
0
yunusumaseko
yunusumaseko :
ndikudikila chithuzi please 🙏
2026-11-23 10:53:13
0
esnart.grivin
Esnart Grivin :
zoonadi brother mzanga anakwela uber kupita kutchito ku Danoon ofikafika pageti ya kuntchito anawatchingila kumutenga driver pagalimoto yake kukamutsekela akuti akalandilre chilango , sitikudziwa kuti amusiya ndi moyo?? mtsikanayo anakamusiya ku tex lank kuti akakwele tex akuti auber akuwatchingila malonda zovutatu.
2026-11-23 10:58:43
0
stan.sandram1
Stan sandram :
ine ndimankhala kuno ku Dunoon near Tax rank area 23 wa tax rank ( koopsa kwambili ku Dunoon 28 side komaso ku 31 side ndi ku 23 side waku Ngenani
2026-11-23 10:44:21
0
edlo.gadafi
Edlo Gadafi :
pa office sindinapaonetu
2026-11-23 10:39:51
0
gown_world_rsa
gown_world_rsa :
ku delft and samora
2026-11-23 11:11:45
0
mapsmaps1900
lover boy :
Date plz isamavute kusaka from today onwards write a date
2026-11-23 11:26:15
0
gladysphunduma
Gladysphunduma :
Ku dunnon ndekuti achimwene
2026-11-23 11:02:45
0
malume.silia
Malume Silia :
🫡🫡🫡🫡🙏🙏
2026-11-23 10:40:42
0
To see more videos from user @imyvoicemalawi, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About