ine uyuyu poyamba sindimkamuvesesa koma srs uyuyu akukamba zenizeni srs awawa nde mawu a Mulungu
2026-11-27 17:56:58
8
Norah Kumwenda :
kod founder wa seventh day ndi ndani mesa ndi munthu
2026-11-27 17:55:17
8
Grace ticheza :
komabe sitikuntha mpingo ndiwomwewo kaya Pali vuto kaya palibe koma mpingo ndiwomwewo sitikuntha sda
2026-11-28 07:06:44
0
King Hecter :
seventhday ine nde singalowe bola kumakamwa mowa wamva
2026-11-28 04:16:45
0
Augustine Lee :
Mpingo supulumutsa munthu bro just do what the bible says
2026-11-28 04:45:00
1
elizabeth :
zonad brathr
2026-11-28 07:08:14
0
Gospel the great :
Mpingo ndi WA yesu basi
2026-11-27 20:35:26
3
zione mhango :
uncle 7 day simpingo koma ndi TSIKU limene mulungu anakhazikitsa kuti TIPUME ndi TSIKU LA number 7 exsodo 20 vs 8 werengani mulungu anakhazikitsa TSIKU LA number 7
2026-11-27 18:24:24
3
Merica Mussa Merica1234 :
sono mpingo wophemberela mulungu uli kut
2026-11-27 21:05:00
1
Abwenzi tiktok :
Ndiye titani?
2026-11-27 18:48:57
3
😇😇 :
Bwanji aliyese azipanga zomwe zamusangalasa
2026-11-27 19:52:16
1
Latifa mahhal :
basi ine ndizipephera ndekha kuchipinda kwanga iyah iwe utitayitsa yesu