lets not judge the people who cant defend themselves since they aint here anymore.😭😭😭 am crying
2026-11-13 10:13:49
213
Damzy :
sono waimitsa coaster choimitsiraso truck ndichani?
2026-11-13 14:53:43
33
Emminence1213 :
kukonda ndalama too much a traffic
2026-11-13 12:03:49
114
Blessings Mathiyah :
ndakhala ndikunena izizi... amaima mu highway kuti azitani
2026-11-13 11:47:25
68
JAMES G motor :
malo awa siabwino kumaimapo a traffic.
2026-11-13 11:16:55
53
puranko :
achitabwino mwina nkuchepesa zoyima musewu!
2026-11-13 11:55:35
16
Billionaire@43💪 :
The problem is that most times amayimitsa galimoto yili pafupi kale not minding the required metres between the car and the officer.
2026-11-13 12:30:58
23
Tendaih :
😭😭😭😭😭 ngati ngozi yomwe inachitika pa Lojwa pa 29 October ya amayi anga kugwa pasi galimoto kuponda kumutu ' kunyenyelatu 😭😭😭😭😭😭
2026-11-13 10:30:27
33
Ayandah :
Za imfazo sizinayende koma kunena zoona a traffic saima Malo abwino,, ayima bwanji pa nsese koma,,
2026-11-13 14:52:01
8
Esther 💞💞❤️💞 :
Eeeee sister in law masilda Banda 😭😭😭😭😭😭😭😭
2026-11-13 11:24:31
26
make Mzati :
ine ku blantyre ndimadabwa nako a traffic amaima malo opanda popanga park
2026-11-13 12:55:30
11
Mkwambahellen :
pena uwapeza abisala pa Conner ku inu apa poima zoona?? ndi anthu ochimwisa mayankhulidwe awa aaaaah! May her soul rest in peace!! imagine ana akhala amasiye
Kodi Mesa amayenera ayambe kuyimitsa from 100Meters?
2026-11-13 13:56:10
6
Amina Osman :
Ohh nooo
2026-11-13 18:15:18
0
martinmedson976 :
aaaaa a police makani basi
2026-11-13 10:20:16
46
BELI :
vuto la a police kuzimva super power
2026-11-13 18:13:24
0
klein🙂 :
nsewu uwu magalimoto amathamanga osat chibwana may her soul rest in peace
2026-11-13 10:20:23
18
Mphatso Pembereka :
Ma Temwa inu😭😭😭😭
2026-11-13 10:53:29
6
user8854269830815 :
Wina ndizamugunda ine adzachimina
2026-11-13 11:08:25
7
Diego :
l don't blame wa traffic pti wakufa salakwa , vuto loyamba Atraffic ku Malawi simudziwa malo oima nthwi yoyimitsa galimoto ,kuimitsa galimoto itafik kale .Umadabwa mu interchange mwaim traffic ati akugwr ma galimoto zachn speed trapp akuti agwr othamang ea kay moyener kuthamanga kumn menemuja .Si galimoto iliyose imayenda pa msewu imakhl ili bwin
2026-11-13 11:39:59
9
Mah🌸🌸🌸 :
Ine tsiku Lina nnazifusako kut Koma zomwe amapanga a traffic enazi ndizibwana olo aona galimoto ikubwela chothamanga amangoti duuu pakat pansewu osasutha eeeeiish zosayenda
2026-11-13 11:04:02
9
Aaron :
zikuoneka kut zomwe mukufotokoza simomwe zinaliri ndipo truck mwina inatha ma break nde yagunda coaster yomwe yagundaso galimoto inayoso
2026-11-13 11:23:49
4
ginte B :
ndikut kodi kumeneku
2026-11-13 12:13:16
0
Samson Nkhoma :
zachitika liti zimenezi
2026-11-13 10:26:06
1
To see more videos from user @_astro_is_that_u, please go to the Tikwm
homepage.