koma nde mwaondat bambo mumadya koma? kapena nkhani za kuchikangawa
2026-11-14 10:43:01
1
cathy kundembe :
Awa sanayakhe zamafita siziku wakhudza
2026-11-14 08:46:18
1
Kabuneti Banda :
kuyankha kwambino
2026-11-20 07:45:20
0
levison moseya :
anthu ena kulemba comment ngati amaphuzila ku school yankaka zosaveka[Laugh approved][Laugh approved][Laugh approved][Laugh approved] koma zoonazake chakwera ndi president wazelu[Pray]
2026-11-14 11:57:59
0
success :
Uyu ndi Doro ka100
2026-11-18 08:39:37
0
Isaac Frazer :
munth wa mkul. 2030 wooooooo!!!!
2026-11-14 11:59:34
0
Miss Thocco :
Nde a kuwona gati azawina akutaya nthawi musiyeni azidyeledwa ndalama anambapochoka mumboma, MCP chisiyileni Kamuzu inawinapo anabwera 2014 kunthamangisa adpp chifukwa cha tonse alliance ku panda ma vote a chilima, mai Joyce Banda, ndi Chihana bwezi akumuziwa Chakwera ndidani ayamike kuzichepesa kwa Chilima kulola akulu amimpigo atawawuza kuti modzi mwa inu agonje asogole modzi chilima anazichepesa kuti asogolere tonse alliance kwa 5years kenako Chilima koma pano Chilima Ana muphwa kufuna so pando nde agalole kusiyila munthu pando gati anaphwa Sindiki minya chifukwa cha pando womwewu nde agatule pasi undido or ku Church ku semblance azake wopikisana nawo amawaphwaso kuti a sale yekha
2026-11-14 12:21:43
0
ZINGAPHELE :
Lazaroooooooooo kkkkkkkk
2026-11-14 15:49:32
0
www.mkwambisi.com :
misala2
2026-11-15 09:57:34
0
@scolaMW :
Kd inu mulipo mafuta samasowa? kagweleni uko akupha
2026-11-14 08:42:15
0
markusmvera :
🥰🥰🥰🥰🥰🥰
2026-11-15 08:47:01
0
user5500778701923 :
🥰🥰🥰🥰
2026-11-14 09:11:18
0
To see more videos from user @winnersonlie1, please go to the Tikwm
homepage.